December 9, 2024

Ochita zisudzo odziwika bwino wamdziko la Nigeria John Okafor kapena kuti Mr Ibu, wamwalira.


Mr Ibu akhala akudwala kwa pakanthawi, ndipo amwalira lero mumzinda wa Lagos kwawo ku Nigeria. 

Mr Ibu ndiwo adadziwika kwambiri mzaka zama 2000, ndipo filimu yoti Mr Ibu anayijambula mu 2004 ndi ana ozunguza omwe amadziwika kuti Aki and Pawpaw mu filimumo.

Kalelo munthu ukamaonera filimu yoti muli Mr Ibu, nanjinanji mukhaleso tiana tosautsato, munthu umadziwilatu kuti apa ting’amba mapapo ndikuseka.


Discover more from KossyDerrickent

Subscribe to get the latest posts sent to your email.

Leave a Reply

Your email address will not be published. Required fields are marked *

Discover more from KossyDerrickent

Subscribe now to keep reading and get access to the full archive.

Continue reading